HOW I BECAME INVOLVED INTO SATANISM(part 5) Patatha miyezi 8 - TopicsExpress



          

HOW I BECAME INVOLVED INTO SATANISM(part 5) Patatha miyezi 8 chiyambireni kugwira ntchitoyi, ndinapita ku church ina komwe ndinali ndi ntchito yoti ndikagwire, ndinatumidwa kuti ndikagwetse mbusa wa church imeneyo. Mbusa atayamba kulalikira thupi langa lonse linagwidwa dzazi. Ndinayamba kumva kuyabwa thupi lonseli ndipo ndinayamba kunjenjemera. Ndinasowa mtendere moyo wanga wonse koma ndinkalephera kutuluka mu church muja, kenako mbusa uja anayankhula kuti " mzimu wa ambuye ukundiuza kuti muno muli munthu wina amene ali ndi ziwanda zoopsa, ndiye tiyeni tonse tipemphere" . Mbusa uja anapemphera zolimba, ali mkati mwa pemphero ndinagwa pansi ndipo anthu onse anali odabwa mene thupi langa linasinthira. Mbusa uja anapitiliza kupemphera mpaka ziwanda zinandichokera ndipo thupi langa linabwelera mwa chikale. Mkazi uja ankapitiliza kumandivutitsa kutulo, nditapita kwa mbusa uja anandipemphelera ndipo ndinalandira mphamvu za kumwamba. I thank GOD dat he saved my life.......... My advic to my fellow young pipo, dont get carried with any gal or boy on facebook, there is more to life than love .
Posted on: Fri, 27 Sep 2013 16:53:28 +0000

Trending Topics



Recently Viewed Topics




© 2015