Malawi wawola. Last week malilo 30 adaola pa chipatala - TopicsExpress



          

Malawi wawola. Last week malilo 30 adaola pa chipatala chomwechi. Dzulo akuti zonyamulila mitembo nzoonongeka, malilo akugoneka pansi , ma shelf adathyoka. Osakonza mavuto onsewa kumangowa yang-anila ndalama mutapangila maphwando k200mn+K65mn kodi amatelo? Lelo tamva kuti mzipatala ma ARV mulibe, ku PHALOMBE odwala AIDS 20 adafa kaamba kosowa ma ARV in 2wks. Ku MZUZU mahule akupangitsa osamwa ma ARV, Malawi on a time bomb?
Posted on: Sun, 13 Jul 2014 22:38:28 +0000

Trending Topics



Recently Viewed Topics




© 2015