Team ya Malawi ikhale ikunyamuka ulendo opita ku Ethiopia kudzera - TopicsExpress



          

Team ya Malawi ikhale ikunyamuka ulendo opita ku Ethiopia kudzera kubwalo la ndege la Chileka.Flames inyamuka nthawi ya 3 Oclock. Sankhani Mkandawire, Micium Mhone ndi Charles Swini awasiya pa ulendowu. Malawi ikuyenera kudzagonjetsa Ethiopia ndiponso kupemphera kuti Mali isadzapambane pomwe ikudzakumana ndi Algeria. malawi ili ndi 6 points ndipo ili pa number 3 potsatira kupambana kwake dzulo pamaso pa Mali ndi zigoli ziwiri kwa duu, zabwino zonse anyamata.........@Andy
Posted on: Sun, 16 Nov 2014 12:16:30 +0000

Trending Topics



Recently Viewed Topics




© 2015