Zochitika PA Cape Town Posts - TopicsExpress



          

Posts by Zochitika PA Cape Town



ZIDAKWA ZAZIKULUZIKULU 10 MU CAPETOWN. #president george
ZIDAKWA ZAZIKULUZIKULU 10 MU CAPETOWN. #president george Mzwale,uyu ndi madala,amamwa mowa modabwitsa,mwana wake weniweni atamwalira iye anakatengapo...
Nkhani ya chisoni. GERALD NGALAUNDE WAZIMPHA. Gelard Ngalaunde
Nkhani ya chisoni. GERALD NGALAUNDE WAZIMPHA. Gelard Ngalaunde yemwe amadziwika kwambili ndi dzina loti Lampardochokera ku Ekwendeni {Mzimba} wanfa i...
#Mzimu ya zochitika,chonde bisani dzina langa,ine ndikufuna ndinve
#Mzimu ya zochitika,chonde bisani dzina langa,ine ndikufuna ndinve maganizo a fans pa page lako ili. Ayise zochitika,nkazi wanga amakonda kwambili ku...
Welengani pangono izi, Monga Zochitika ndinapeza mwawi mkucheza
Welengani pangono izi, Monga Zochitika ndinapeza mwawi mkucheza ndi Makwinja iyeyo osadziwa zoti ndine. Mukucheza kwathu ndinamudziwa Makwinja ndipo ...
Monga Zochitika sindinalephele kufufuza mbiri ya (MILIAM) mkazi
Monga Zochitika sindinalephele kufufuza mbiri ya (MILIAM) mkazi yemwe wakhala akuyambanitsa (SIKINALA ndi MAKWINJA). Umu ndi momwe ndapezela kambili k...

Trending Topics




© 2015