AKUFUNA KUTI KUMPOTO LIKHALE DZIKO LOYIMA PALOKHA NDIPO - TopicsExpress



          

AKUFUNA KUTI KUMPOTO LIKHALE DZIKO LOYIMA PALOKHA NDIPO KUZITCHEDWA NORTH MALAWI!!!!!!!!! Pamene dziko la malawi likukondwelera kuti papita zaka Makumi asanu chilandilireni ufulu odzilamulira kuchokera kwa azungu, anthu ena akufuna awononge chikondwelerochi. Anthuwa ndi ochokera kuja ku chigawo cha kumpoto kwa dziko lino omwe akuti ali kalikiliki ndi ma plan ofuna kuti chigawochi chikhale dziko loima palokha. Akufuna kuti dziko lawolo lidzitchedwa Northern Malawi. Tiuzeni Zoona kodi kumpotoko kulichani chomachita kunyadira chonchocho nanga inu mukugwirikananazo??? Tiuzeni zoona
Posted on: Sun, 06 Jul 2014 07:57:26 +0000

Trending Topics



Recently Viewed Topics




© 2015