Admin plz tauza anthu agroup lakoli andithandize vuto langali - TopicsExpress



          

Admin plz tauza anthu agroup lakoli andithandize vuto langali chonde! Ndine mnyamata wazaka 30 ndimakhala ku Lilongwe ndilindi ndimkazi okongola heavy! Ndi mwana modzi wa mamuna,ikakhala gele ndiye ndinavaya nayo patali kwambiri mwakuti ndili ndi degree in Civil Engineering! Yomwe ndinathatha pa polytechnic! Mwana wanga panopa akugera ku Karibu Acadamey! Mkazi wanga akuvepa ku migration! Ineyo ndinatsegula Chi shop chachikulu mu LLs,chofanana ndi cha amwenye! Munthune ndimafuna mundithandize chifukwa vutoli ndilakale kale silikutha ngakhale anthu anayesetsa kundithandiza,m wina kapena anthu agroup ino mukhoza kundithandiza,chifukwa nzanga winanso akuti munamuthandiza ndipo vuto lake linatha,ndiamene wandiuza kuti ndiyese pano !vuto lake ndilakuti munthune sinditha kusunga chinsinsi! Mwakuti 2019 ndidzavotera DPP!
Posted on: Sun, 03 Aug 2014 15:05:01 +0000

Trending Topics



Recently Viewed Topics




© 2015