Amen Amen Amen Amen it has done perfectly wow wow at OSSAC GOD - TopicsExpress



          

Amen Amen Amen Amen it has done perfectly wow wow at OSSAC GOD glory b 2 u only me susan ma shema wa Dkudzala zachitikadi mwa Ambuye, I thank God posanditaya ndimkafunitsitsa caterin wen i was at Malawi but i never make it luky of ndalama i remember Vic Banda 4rm kabula livin waters u tried 2 help kuyangana malo axul at tradefair koma ndinalephera koma Mulungu si ine ayi iyeyo ndi Mulungu basi sadzapezekanso wina ndaona ine ukulu wake ndiwazotheka. Alemekezeke yehovayo,the class of 40 pple with three Malawians God choose me 4 the caterin speech ine mkuima pachinamtindi cha wathu at Luwis kuper hall zimene sindimayembekezera kuima pakati pa azungu ma blak amzanga lemekezekani Jehova ndinu nokha mukule mu zonse ndipo ambuye mutsiriza mwachiyambachi its ma prayer 2 u God.its hapenin here SA MUKULETU basi Ambuye
Posted on: Thu, 28 Nov 2013 21:37:27 +0000

Trending Topics



Recently Viewed Topics




© 2015