Anyamata ena lero amalozerana mkazi wina wake amvekere chick iyo - TopicsExpress



          

Anyamata ena lero amalozerana mkazi wina wake amvekere chick iyo aise inagwidwa ndi kape koma kaya bwanji kaya sindimamvetsa... Hahaha ndinangoseka. Amuna lero timvanepo apa. Mukaona mkazi akukakamira mwamuna amene ambiri mumati si type yake, mukadzamuona mkazi kulolera kukwatirana ndi mmphawi ngakhale mkaziyo kwawo mkochita bwino... Mkazi akadzati wakana achuma ndikulora mwamuna onyozeka kugulu kwa anthu.... mudzangodziwa kuti mwamunayo ali ndi umunthu ndipo mkaziyo amapeza naye chimwemwe ndi mtendere wamumtima..... Amuna ambiri ali mvuto, amadzimva kwambiri kwa mkazi wawo, safuna kugonja ngakhale alakwe. Safuna kudekha, sakhala ndi mtima omumvetsetsa mkazi ndikugawana maganizo ngati anthu amodzi. Amuna ambiri sakhala ndi nthawi yoti amukonde mkazi wawo... Shame! Most men act so crazy when it comes to Love, they treat a woman as if they are both men. Often times they dont event respect her, kenako umangomva kuti mkazi uja wapita, ena mkumati wachokeranji iye uja nkhuku zimadyedwa kumene kuja, magalimoto mbwembwembwe. Sichina, iye amafuna CHIKONDI... Ndidule nkhani: Ukhonza kumatchena, kumayendera galimoto yodula, kugwira ntchito yapamwamba koma ngati ulibe chikondi kwa mkazi wako, ULI CHABE, u r just a useless Man.... THATS HOW THE STORY GOES! You will never feel the love of the natural woman. A natural woman, need to be LOVED not your money... Sounds strange but its TRUE. Sinthani mkhalidwe, learn to love and shes gonna be yours FOREVER!
Posted on: Mon, 11 Nov 2013 18:16:25 +0000

Trending Topics



Recently Viewed Topics




© 2015