BLANTYRE PRESS CLUB: Blessings Petit Kanache: 20 hrs aziwa liti - TopicsExpress



          

BLANTYRE PRESS CLUB: Blessings Petit Kanache: 20 hrs aziwa liti kut mu envelop yawo munali ndalama? And zomwe akukabwezazo, ndi ma bank notes ake anatenga ku sanjika? Kapena anadikila alandile kaye salary? Bwanji sanabweze ali ku sanjika tsiku lomwelo? Kapena akudelela kuti ndalama yachepa mwina ikanakhala 2 hundred thousand kwacha? Reporter yemwe sanalandilepo allowance ndi ndan? Awa ndi mafuso akufusa anthu omwe ali kuno ku zomba pa function yomwe ndili, ndusowa mayankho. Rejoice Nasimango Shumba: hahahahahahaha Blessings Petit Kanache mwati akufunsa ndi ndani & kutiko lolest?? By the way inenso I have the very same sentments. Chakula apa nchakuti anthuwa akuidelera ndalamayo osati za bribe they want us to believe zo. 20 hrs · Like · 3 Maya Gloria Kafwamba: kodi kuma function a mabungwe ena sitimalandilako kkkkkkkkk 20 hrs · Like · 1 Gusto Mulomole: Mayankho ulinawo iwe Bule...apatse amenewo. Nde mwati ndalamayo anayamba kaye ayigwiritsa ntchito uku akudikira salary kuti ilowe? hahhahaahh, nawonso amakhala mmaluzi eti? kkkkk... 19 hrs · Like · 1 Mercy Chaluma kodi ena akubweza? kkkkkk.. mmene ankalandira ma envelopewo ankati muli ma notepad? pretenders! 19 hrs · Like · 5 Edith Mkwaila adya zingati za anthu a ndale? chifukwa apa apeleka ma share ofanana ndiye lero awoneke holy holy? iiii basi ndasiya ndngalankhule kuyipa 19 hrs · Like · 1 Blessings Petit Kanache kikik bwana Mulomole, mayankho ndilibe, ndagwidwa njakata kuno ku Zomba, kapena tawayankheni anthuwa inuyo, kikik @ Rejoice, kuno ku Zomba, lol @ Gloria, izo nzomwe akudabwa anthu kuno, @ Mercy, ai, palibe wabweza koma akuganizaaaa? Ena kukhala ngat.... kuno ku Zomba, ena akuti mwina kuzolowela ma 2 pin ku ma function? 19 hrs · Like Blessings Petit Kanache @ Edith, kikik koma ndiye ma share ma share 19 hrs · Like Chembezki Velepi Mhone Moti izi zili mmanjazi ndibweze???? Not in this lifetime. 19 hrs · Edited · Like · 2 George Maida Fumwe mafunso mufunsa ndinu osati anthuwo? Tangosainani mudzibwera. 19 hrs · Like Simeon Shumba Tikawonana ku NAMISA ine kupita kunyumba yamfumu kukandiphera nkhuku then popita kundipats mbuzi is it wrong?chikhalirecho kukhala koyamba what a nonsense.Thats why we are saying we need to remove this gap mu Media otherwise anthu adzatifinya awa its our time to change things vote wisely zitsanzo mwayamba kuziona nokha 18 hrs · Like · 1 Blessings Petit Kanache Chembezi, not in this life i agree, hahaha @ fumwe Maida, mafunso akufunsidwa ndi anthu ena kuno ku Zomba, ndithu 18 hrs · Like Blessings Petit Kanache @ Shumba, you have said it all, zimveleni mu ntolo atola nonse 18 hrs · Like Chiku Jere Pulezidenti wapelekera pambalambanda osabisa bwanji osakabwenza zomwe amalandira kuseli kamabwana ena? Ka fifite ndiye kubwenza koma zikakhala phwamwamwa zamu mdima ndiye kuthyolera nthumba. Kabwezeninso mafiliji aja kikikiki! 18 hrs · Like · 1 Rose Chipumphula Akubweza chifukwa zachepa?sanabweze bwanji tsiku lomwe analandilaro? mwikho 17 hrs · Like Deus Sandram Kutereku inenso ndili kufunction andipatsa 47 pin, ndawauza kuti ine ayi, anthu angayambe kunditukwana, ndakana, ndikufuna kukhala mtolankhani wachitsanzo! 15 hrs · Like · 3 Chikondi Mmanga Kasambara Deus Sandram choka iwe okonda ndalama ngati pali nkhope yako ungabweze iwe iyaaaaaa! 15 hrs · Like · 1 George Mkandawire shame 15 hrs · Like Christopher Sande kkkkkk koma guys eeeh ai vuto lake anthu ena akalemera they want to pretend kuti they have not been getting ziponda yet........ 15 hrs · Like · 3 George Mkandawire A sande mwati timalandira kamba ka umphawi or kupanga deserve? 15 hrs · Like Godfrey Maocha I wasnt at Sanjika but to agree with Edith Mkwaila some were not happy that editors and mere reporters were given the same amount asa 15 hrs · Like · 2 Rose Chipumphula Maocha sanawapatse zofanana ena analandila 14 hrs · Like Hastings Jimani i was not there but mukutitukwanitsa zinali zingati kodi ena kuti K40 ena K50, ena akuti K30 ena K90 guys zinali zingati of course nanenso ndikana......... ndinakapitako........... 14 hrs · Like Vicky Victor Junior Singano Paja kuli mavoti,, mnayiwala,, hahahahahahaha 14 hrs · Like Godfrey Maocha then ama 100 abweze.to agre with one Simeon Shumba vote wisely ku NAMISA some have never been reporters sadziwa zikhomo. 14 hrs · Like Rose Chipumphula Ku NAMISA tikavota mwa nzeru 13 hrs · Like King Franklin Mtambalika Tivote zimenezi mwanzeru 13 hrs · Like George Mkandawire Kodi Godfrey Maocha Vito ndi kusauka? Simeon so u mean we should continue getting allowances instead of improving our welfare as journalists? 13 hrs · Like Tikondane Vega allowances cannot hinder you from being unporfessional. you guys i thought you know your job? 12 hrs · Like
Posted on: Thu, 27 Nov 2014 05:04:39 +0000

Trending Topics



in-topic-816998318338510">Prophecy for 2015: 1) Crown of righteousness for us in

Recently Viewed Topics




© 2015