BREAKING NEWS! Grace chinga RAPED just Now! Mvula ikakuwona - TopicsExpress



          

BREAKING NEWS! Grace chinga RAPED just Now! Mvula ikakuwona litsiro sikata..... Grace chinga mzimai oyimba nyimbo za gospel ameneso pano ali ndi mimba ya Josephy Tembo, amugwililira usiku omwe uno pamene amakagula airtime kuti amuyimbire mwana wake amene akuti wadwalika kwambiri. Pakali pano mai chinga awatengera kuchipatala komwe akukalandira chithandizo. Apolice agwirako amuna awiri powaganizira kuti ndiwo achita zachipongwezi. More to come.....
Posted on: Wed, 10 Jul 2013 21:36:35 +0000

Recently Viewed Topics




© 2015