DPP INAPITA NDI MALEMU BINGU WA MUTHARIKA, Aphungu awiri achipani - TopicsExpress



          

DPP INAPITA NDI MALEMU BINGU WA MUTHARIKA, Aphungu awiri achipani chotsusa boma cha DPP, Afredrick kamwangala aku Lilongwe North west ndi Agnes Penemulungu aku Lilongwe south, Dzuro alengedza kuti atuluka chipani cha DPP, Ndipo apempha Speaker wa nyumba ya Malamulo A Chimuthu Banda kuti awapatse malo mbali yomwe imakhala aphungu oima paokha. Aphunguwa ati atuluka Dpp chifukwa chipanichi chilibe tsogolo lililonse. Zeze
Posted on: Tue, 25 Jun 2013 04:53:03 +0000

Trending Topics



Recently Viewed Topics




© 2015