Dear all, if u know th@ i invited u to my engangement and u didnt - TopicsExpress



          

Dear all, if u know th@ i invited u to my engangement and u didnt come dont waste time and ur cards inviting me to ur function,whether an engangement or wedding pamaliro panu sindizabwelanso(lol).koma seriously i go for an eye for an eye.ngati inu simunabwele ine sindingabwelenso unless other wise,mwina mutamatumiza invitation yanuyo ndi explanation yomveka bwino supported by a medical report yosonyeza kuti mumadwala kapena death certificate yoikila umboni kuti munali ku maliro.shupiti,ana a ana anjoka inu
Posted on: Thu, 24 Oct 2013 11:00:37 +0000

Trending Topics



Recently Viewed Topics




© 2015