"FLAMES NDI TIMU YOPEPERA,MPHALE" -Saintfeit. Mphunzitsi wopuma - TopicsExpress



          

"FLAMES NDI TIMU YOPEPERA,MPHALE" -Saintfeit. Mphunzitsi wopuma wa Flames a Tom Saintfeit wati kutula kwake pansi udindowo,sikuti iyeyo ndiwolephera ai: koma kuti timuyi ndi "yokanika" Mkulu waku Belgium amalankhula izi ndi mtolankhani wa wailesi ya BBC dzulo. Mwazina Saintfeit wati mwa matimu waphunzitsa iye Malawi ndimene ili mphale "vuto si langa koma ma player kusamva,kuphunzitsa umu ndi umu osatheka" Mkuluyu adalembedwa ntchito mu njira imene idadabwisa anthu miyezi yapitayo. adminKATAKWE wa MNEG kuno ku Blantyre.
Posted on: Tue, 10 Sep 2013 04:45:49 +0000

Trending Topics



Recently Viewed Topics




© 2015