Flames imadzimva kutha mpira hevy #Namzy Timu yoti nthawi - TopicsExpress



          

Flames imadzimva kutha mpira hevy #Namzy Timu yoti nthawi zambiri simachita bwino koma nthawi zonse nkumalowa mu camp mochedwa nkumati mukufuna kupambana?.Kupita ku Mali opanda friendly game zoona,mumaona ngati mukasewera ndi Djibout?.Nthawi zina ikapedza ma friendly game nde kuti Tanzania,Zimbabwe atithandidza chani pomwe anzathu oti ku Afcon amapitapita amaitana matimu amphamvu chonde a Fam muunikepo pa zatsogolo la timuyi. Ma local salibwino kuposa ma prof?. Ma prof ena sakusewera kunjako ndipo mu camp ya flames amangokharamo tsiku limodzi koma kupasidwa game?.Tiyeni tiyikenso chikhulupiliro mwa local players atha kuthandidza tisangofera zoti auje ndi a profe yet munthu anapima. Kumenya defending koma kumagonjanso!! Munakapanga defending ku Benin koma anakakupulani,mwapita ku Mali mwakapanga defending mwakwapulidwanso nde cholinga chanu ndi chani poti mukasewera attacking kwathu kuno palibe chomwe mumachitanso.Ma coach opanda chikhulupiliro ndi timu yanu inu.Ethopia ifika lero game ndi la chitatu kaya
Posted on: Mon, 08 Sep 2014 04:29:21 +0000

Trending Topics



Recently Viewed Topics




© 2015