GOOD NEWS TO OUR RED ARMY SOLDIERS!! Akulu-akulu athu(EXECUTIVE) - TopicsExpress



          

GOOD NEWS TO OUR RED ARMY SOLDIERS!! Akulu-akulu athu(EXECUTIVE) anenetsa kuti Game ya Lero akuyitenga ngati FINALS nde alonjeza kuwakwezela ma PLAYER Malipiro(GAME BONUS) aGame imeneyi akawina. Komanso Ndalama yomwe aTNM amapereka kwa #1 wa 1st Round(MK250,000.00) ma PLAYER azawagana Yonse okha. Komanso Pali Chiyembekezo choti Malipiro ama PLAYER akufuna awakwezedwe kamba ntchito YOMATANDIKA yomwe akuyigwira anyamatawa.
Posted on: Sun, 20 Jul 2014 05:29:21 +0000

Trending Topics



Recently Viewed Topics




© 2015