Guys ndithandizeni maganizo eti munthu wangolowa - TopicsExpress



          

Guys ndithandizeni maganizo eti munthu wangolowa kumene pa facebook(ndi mtsikana friend waku hood kwathu),,ali ndima friends awiri wina ndineyo wina ndi brother wake nde status yake yoyamba wangofikila kuti Usiye kundilonda sindidya kwanu,ndipo sindimakufuna,m phawi wachabechabe ngati iwe ungandipase chani,kapeze akazi a level yako nde guys its obvious sakunena brother wakeyo nde ineyo zundipweteka,,, ,will it be proper kuti ndingomuyankha or ndingozisiya ndiyisove basi.......ndim angocheza naye sindimamufuna
Posted on: Thu, 15 Jan 2015 09:19:18 +0000

Trending Topics



style="min-height:30px;">
Sabes que has jugado mucho a Resident Evil cuando... 1.Piensas
Diving Indonesia just became that much more awesome! In
Siamo is back with Free Pizza Wednesdays! An interactive game

© 2015