Ine ndinkaotha dzuwa tsiku lina pa khonde pakwathu, nde padabwera - TopicsExpress



          

Ine ndinkaotha dzuwa tsiku lina pa khonde pakwathu, nde padabwera mzungu wina anvekere, Mzungu : are u reluxing? Ine : no, am Dj Zimbabwe MW. Mzungu uja adangonyamuka nkumapita,posakhalitsa padabweranso ka nkazi kenakake,kanekere.. Kamkazi : Hey man, are u reluxing? Ine : No am not girl, am the Dj,do u mean u dont knw me? Ndimaimbanso, Kamkazi : wow i c, i thougt u are just reluxing.. Kenaka ndidalowera chaku ground,ntafikako ndidapeza man ena ake atakhala pa kamwala koma nkhope yawo idali ya chilendo kwaine, mmalingalilo anga ndidaganiza kuti akhoza kukhala a reluxing akufunidwa aja,kenaka ndidawafunsa.. Ine : man are u Reluxing? Man aja : yeah broh,u just know i am reluxing.. Ndidaphya mtima ndipo ndidampatsa khofi.. Ine : iwe anthu akhala akundivutitsa uku ine kumandifunsa if am reluxing iwe uli phee pano? Mbuzi yamunthu iwe eti,kusonyeza kuti iwe ndine timafanana mutu wake umenewo? Mxiew One word 4me...lol #DjZimbabwe.MW
Posted on: Mon, 11 Aug 2014 13:12:30 +0000

Trending Topics



Recently Viewed Topics




© 2015