Jucky Juma > Malawi breaking newz and dating Kumalawi kuno - TopicsExpress



          

Jucky Juma > Malawi breaking newz and dating Kumalawi kuno kuli mitundu ya anthu yosiyana koma yotchuka ndi itatu 1ayao 2achewa 3 atumbuka komatu osewa amaziwika ndizitchito zawo. Ayao amaziwika ndi bisnes. Achewa ulimi. Atumbuka maphuziro koma pa onsewa ochenjera ndimuyao chifukwa amatha kukwatira mtundu ulionse malawi muno koma awiriwa amakwatirana okha okha komasotu muyao amafika pamalo ngati ophunzira koma ili mbutuma yeniyeni. Ngati pali waumbombo 1 ndimtumbuka. Ufiti kaduka nchewa kukonda azimayi ayao pitilizaniko
Posted on: Tue, 13 Jan 2015 15:19:23 +0000

Trending Topics



Recently Viewed Topics




© 2015