KALATA YOPITA KWA BAMBO L.NTABA OLemekezeka..kalatayi sizot - TopicsExpress



          

KALATA YOPITA KWA BAMBO L.NTABA OLemekezeka..kalatayi sizot ndangolemba mwachibwana ayi koma ndikuimirila athu onse omwe anaona mkwiyo wanu ku simba kuja...,,#mr_condom ... Wadahdah #lazy komanso nd ena ambiri omwe sindingathe kuwatchula. Kubwera kwanu ku simba kuja zinari zonyadixa kt tikapita kumpira athu akafuna kutmenya..tizithawira kwa inu ngat mtetez wanthu., koma phuno salota timakhalira limodz mugulu lothawa uku tikulira... Koma tikafika ku simba kuja ndiye munali kuopedwad muthu akangokuputan khan zazingono mumakhala mwa mfinyiratu mpaka muthu kukanika kumedah. Koma chachikulu chomwe ndifuna ndikuziwisen ndi chot pano nafenxo ndima paudalaaa ngakhale bambo #BIG_DAWG avomeleza kt ndifed chimphona...pano ndiye titha kumagemulana njee kuopsezana;;:, ndatha ine, €₹¤ vatcan kid. (#zongocheza_izi_xizamilandu)
Posted on: Thu, 25 Sep 2014 10:04:52 +0000

Trending Topics



Hey guys Here is a bit of the recap from last nights
A woman was pregnant and went to deliver in one hospital.more than

Recently Viewed Topics




© 2015