KUMASULANA TSOPANO!!! Mitundu ya anthu ofoyila pa - TopicsExpress



          

KUMASULANA TSOPANO!!! Mitundu ya anthu ofoyila pa facebook. 1.Pali kagulu aka komwe kamati akamapita kwinakwake nkumalemba kuti Lilongwe loading e.t.c izi ndizachimidzi kwambili,aim yake imakhala yongotiziwitsa kuti iwowo akwelako galimoto. zithe izi. 2.Nde pali ka gulu aka komwe kamamupanga tag munthu zinthu zomwe wina sizikumukhudza. izi ndizachimidzi.popanga tag,imakufusa kuti whom were you with kenaka iwe nkumapanga tag anzako oti panalibe.smh. kumapangana tag anthu oti mumavana komaso mukuziwana,osati poti mwangoona kuti manje ndi dolo basi muzimupanga tag chilichonse.zithe zopanga tag mwaumbuli. 3.aaah ndinaiwala kagulu aka komwe kamangopanga like chilichonse ndi zinthu zopusa zomwe. Celeb asangolemba; i wanna take a bath. dzima like mbwelekete mpaka nde what are you liking? kuti akasamba somhw kumaona stuff yopanga like. 4.Bebi inayake isangopanga upload pic itangojambula chithuzi chakumdima komaso chosaoneka bwinobwino nkomwe makamaka ma camera awa amapanga ngati kunali fog,basi inutu ma coment ma like mbwelekete zinthu zosaonekaso bwinobwino. kumaona zopanga like,ngati liking ndi deal. 5.Nde pali anthu awa omwe amakonda zopanga upload tizithunzi tawo daily.izi ndizachimidzi.mumazikonda ndiinu atsikana.same face,same hair style,same clothes , same jewely,same smile but in different pictures.ahhh ife timatopa nkumakuonani daily.basi paliponse mulipo mangoganiza basi zozijambula? zithe izi tinkhope tanu tokwilimbilato ife mmanso mwathu tinatikola. 5: Pali akazi ena mumati listening to beyonce in bed , eating Chocolate chonsecho mukutakasa thobwa mu bigiri kuti muzizilitse kukhosi kwinaku mukutidandaulira tiana tosasamba takwanu kut lasasa... Zithe izi osamatinamiza. Ngati mukupita kumunda kumanena apa osati ndili kubridal shower Kkk ndatukwana apa zinazo wonjezerani!!!!
Posted on: Fri, 19 Dec 2014 07:04:43 +0000

Trending Topics



Recently Viewed Topics




© 2015