KWA ANTHU ONSE AMENE AMADANDAULA ZA SQUAD TINAIKA DZULO TINAPANGA - TopicsExpress



          

KWA ANTHU ONSE AMENE AMADANDAULA ZA SQUAD TINAIKA DZULO TINAPANGA POST IZI; THE PEOPLES TEAM IKHALA IKUNYAMUKA MAWA. Pali ma player ena atsopano amene team yatenga.. #Wisdom_Minze y ( mphwake wa fisi matama - ) #Yamikani ________ ( striker) Komaso Ma player Ena amene ma page ena akhala akukunamizani kuti sapita.. Iwo ali nawo mu ndandanda wopita chifukwa amapanga nawo zokozekela ndi team #Owen_Chaima #Douglas_Chil ambo #Chimango_Kai ra #Dalitso_sair es #Sankhani #George_nyire nda ( anapita kumuzi kunachitika maliro ) tizakupasilani ndandanda ose mawa pamene team izizanyamuka #YO
Posted on: Fri, 20 Sep 2013 07:22:29 +0000

Trending Topics



Recently Viewed Topics




© 2015