Koma ena kumalandira enafe ayi, chiri chiyani chimenechi? Mukuona - TopicsExpress



          

Koma ena kumalandira enafe ayi, chiri chiyani chimenechi? Mukuona ngati mavuto ife tiribe? Ma leave grand komaso rural allowance ikutisemphaso bwanji ndekuti? Kapena sindilimbikira ntchito? Zimezitu mudzatitemetsa kwa angongole chifukwa ena kulandira ine ayi aziona ngati ndine kapsala ndithu. Ndikadakhala pa lendi ndiye ndikadayaluka chifukwa ma landlord sayimva masiku akamatha chonchi! Ndikunena inu ku Capital Hill
Posted on: Sun, 29 Sep 2013 05:03:46 +0000

Trending Topics



Recently Viewed Topics




© 2015