Ku inbox kuli mafunso ambiri okhudzana ndi Manoma,ambiri mukufuna - TopicsExpress



          

Ku inbox kuli mafunso ambiri okhudzana ndi Manoma,ambiri mukufuna kudziwa ngati sulom yapeleka chigamulo ku Manoma. Ma page ambiri akuti sulom yapeleka chilango ku Manoma koma ili ndi bodza. Sulom sinalandire report kuchokera kwa Francisco Scova, Match commisioner komanso a Blantyre police ndipo akalandira report,akumane ndikukambilana za nkhaniyi. Wina asakunamizeni kuti Wanderers ayiletsa kusewera pa stadium kwa miyezi isanu ndi itatu (8). Chigamulo sichinapelekedwe.......@Andy!!!
Posted on: Tue, 02 Jul 2013 18:33:01 +0000

Trending Topics



Recently Viewed Topics




© 2015