Lero tikambilane ndi anthu a kumpoto kwa Malawi. Anthu inu ambiri - TopicsExpress



          

Lero tikambilane ndi anthu a kumpoto kwa Malawi. Anthu inu ambiri munali a nzeru ku school koma chifukwa ma kampani ali pakati ndi kumwera munakhazikika zigawo zimenezi ndipo kumudzi simufunako. Kodi inu mukatukula kwinako, kumpoto atatukuleko ndi ndani? Chikangawa amaliza anzanu kugwesa mitengo, mvula ija yathawa, nyama zija zathawa, kukongola kuja kwathawa, posachedwapa kumpoto kufanana ngati ku Thyolo. My advice to educated northerners…please meet as a group regardless of your political affiliations and map the way forward. It is not too late. The north has a great potential for growth, but your leaders betray you. I will not mention names. These people want you during campaign period, other than that you are left aside. Please call for job creation in this region to help the youthful and fresh graduates. Cassava can be processed into export products should you have factories to process the crop. You have the brains, please take it to use. Do not wait for left overs from THEM. Other than Kamuzu’s developments, the region is lagging. I know someone will mention about the long overdue Reserve Bank, but I will respond
Posted on: Thu, 10 Jul 2014 22:30:32 +0000

Trending Topics



Recently Viewed Topics




© 2015