MNK: Mayi takupezani kuno kunsanje kumene madzi asefukila, kodi - TopicsExpress



          

MNK: Mayi takupezani kuno kunsanje kumene madzi asefukila, kodi inu mutuzapo chani? Mayi Nadimba: shiiii..Ndidangovambo kuti pwatapwata, mvula yayambambo. Kenako batchi kuyamba kukokolola anthumbo, manyumbambo, kuphakijila aponso jiweto jontche. Mtola Nkhani: nde inu ndokhuzidwa bwanji ndingozi imeneyi? Mayi Nadimba: ndine okhujidwa chifukwa nyumba imene ndimadalira yagwa Ntola nkhani: nde mawu anu ndotani ku ntundu wa a Malawi Mayi Nadimba: Inembo pano ndikuti Amalawi anjanga nonse, kukhala kunsanje nkokoma jedi! Inembo pano tchindinajiwe kuti ndijaikwelambo nkholokopitala. Komambo lero aboma abwera ndi ndege imeneyi nkujatitenga ife. Ambuye amayankhadi. Haaaaahaaaa a nsenafe sitizatheka
Posted on: Fri, 23 Jan 2015 18:02:08 +0000

Trending Topics



Recently Viewed Topics




© 2015