Ma team amphepete mwa nyanja ku salima aimika manja mwamba, agwada - TopicsExpress



          

Ma team amphepete mwa nyanja ku salima aimika manja mwamba, agwada komanso apepesa ku nyerere zamanoma zochokera ku lali luban airbone rangers de flying soldiers yaona ngat kumaloto pamene yachita iwo ngoz pa chitowe ground, ma parachute a airbone aphulika io mmalele ndi mwala omwe wawagenda sparow msowoya, jombo, uniform, piston, ak 47, parachute, zonse izi tengan atero anyamata a airbone kupereka kwa nyerere zaku lali lubani, sparow msowoya anatumiza uthenga ku mafco kut apitiliza pomwe wapanga dzulo ndipo apanganso lero ndipo zathekad, nyamata otchedwa sparow anachita kutumizanso uthenga ku sulom ndiku fam kut akamapanga log table lero pamene pali wanderers aonjezerepo phwamwamwa wama points atatu omwe wanyamula iye ndikuheda pa chitowe. Ndimene zathera kut ku chitowe tatengako 6 points. Mulungu inu mukule ife tichepe. OVINA SHUBEKE PA CONA AKACHINYA, AZAVINANSO BOLA OSASINTHA STYLE YOZINIRA #LICKY
Posted on: Sun, 20 Jul 2014 16:15:35 +0000

Trending Topics



Recently Viewed Topics




© 2015