Morning- Guys atiyeni ku chisankho cha 2014 - TopicsExpress



          

Morning- Guys atiyeni ku chisankho cha 2014 titasukusulapo...ki ki ki ki Seriousily, zoti ine kapena iwe ndi wachipani chanji zitayeni, koma atiyeni tithandizane kuunika kuti kodi mpaka liti Malawi adzakhala akubeledwa ndi kupondelezedwa ndi kagulu ka anthu kochepa panene ife ambiri tili kulimbana tokha tokha? Kaguluka kamasokoneza ku UDF, DPP, lero kali ku PP! Kapena enanu mpaka lero mudakaganizabe kuti akuba ndi kupha ndi maina azipaniwo?? Hell no! Koma CHOWAWA ZED ndichakuti chipani ichi kapena icho tikachivotela chidzalolanso anyapala aja kubweleramo, anthu okuba mopanda chisoni olo manyazi! Atiyeni tichotse anyapala oterowo muzipanimo kuti ambiri adzathe kusangalala nafe. Pomaliza, pepani enanu ndakupangani tag mpaka kangapo (eish, zigoba 3 much!)
Posted on: Tue, 12 Nov 2013 07:41:47 +0000

Recently Viewed Topics




© 2015