Moya amayenda akuyankhula yekha kuti ambuye mutandipatsa - TopicsExpress



          

Moya amayenda akuyankhula yekha kuti ambuye mutandipatsa ten milion ndikhoza kukupatsani one million, kenako anati ambuye mutandipatsa one million ndikhoza kukupatsani one hundred sauzande, akuyendabe anati ambuye mutandipatsa ten milllion ndikhoza kukupasani one million, mutandipatsa one thousand ndikhoza kukupasani one hundred, kenako moya anatola nine hundred kwacha, u know what moya said ambuye ndinu ochenjera mwachotselatu hundred kwacha yanu kkk
Posted on: Sun, 24 Nov 2013 19:05:45 +0000

Trending Topics



Recently Viewed Topics




© 2015