Musabise ma id, Ine ndine leo ndikudandaula zomwe wachita - TopicsExpress



          

Musabise ma id, Ine ndine leo ndikudandaula zomwe wachita #skeffa_chimoto potulusa nyimbo yomwe imayenera kukhala tittle album yanga yomwe ndimayembekezera kutulutsa next year.#skeffa atabwera ku capetown kuno ndidamulongosolera za project ya chimbale changa ndipo adamvera demo ya nyimbo ya chidamuluma chokuda yomwe ikuvuta mu album yake pano.Atamvera adayamikira osadziwa kuti pansi pamtima anali ndi chiwembu.Mau anga omaliza kwa mnyamatayi ndi akuti chomwe adalemba mulungu kuti chidzakhala changa chidzakhalabe changa.. #advisor02
Posted on: Mon, 11 Nov 2013 12:41:02 +0000

Trending Topics



Recently Viewed Topics




© 2015