Mwakhala pachibwenzi over 5yrs ndipo munagwilizana kuti - TopicsExpress



          

Mwakhala pachibwenzi over 5yrs ndipo munagwilizana kuti mudzakwatilana, mumakondana heavy ndipo abale a mbali zonse ziwili amagwilizana bwino.. Yakwana nthawi yoti mukwatilane mwagwilizana kuti mukayezese kaye magazi ndipo mutapita koyezetsa a Doctor apeza kuti wachikondi wakoyo ali ndi HIV+ koma iwe ulibe..... Ungata?? 1. Kukwatilanabe? 2. Kuthetselatu chibwenzi pompo? 3. It depends? 4. Others K£rnel The
Posted on: Mon, 28 Jul 2014 11:43:52 +0000

Trending Topics



Recently Viewed Topics




© 2015