Mwazuka ndiwa mkaka!!! Kulu wa team ya Blantyre united Mr - TopicsExpress



          

Mwazuka ndiwa mkaka!!! Kulu wa team ya Blantyre united Mr Nakoma adandaura ndizomwe akupanga akulu akulu athu posapereka ndalama za loan ya Tizgowere kumwenda ndi Victor Limbani. Anakoma achenjeza team ya bullets kuti ngati sikwanilitsa pomafika second round ya super league tisayembekezere kuwagwiritsa ntchito anyamatawa , iwo apereka chisanzo cha Abraham kamwendo yemwe paka pano sakusewera mpira kamba ka utambwari wa team ya Wanderers Fc. Poyakhapo akulu akulu athu via inbox angoti relax Jabu!! Eshiiii mukhani zina!! Akulu akulu a team ya wanderers fc ali ku Zomba kuthandiza ma practice team ya Zomba united cholinga yizagonjetse bullets fc, yemwe watitumizira khaniyi yemwe ndi m bale wake wwa coachyo , wati anaona modzi wa ma coach awanderers dzuro akupangitsa ma practice team ya zomba united cholinga cholinga choza gonjetsa bullets fc!! Zimachitika mpira sikoyamba, zambiri ndikupasira mazuro !!! In God we trust!! Mawa wa bwino!! Mr Jabu love you all bullets sapotaz!!
Posted on: Wed, 30 Jul 2014 04:29:30 +0000

Trending Topics



Recently Viewed Topics




© 2015