NDI INA YAKE LYRICS INTRO Blakjak- Indee! (GD) Nthawi ina - TopicsExpress



          

NDI INA YAKE LYRICS INTRO Blakjak- Indee! (GD) Nthawi ina yake timazamenya ina yake umadziwa Ndi ina yake koma eti,,, Indee! Eeh! CHORUS Tsiku lina lake/ Ndili pena pake Ndili ndi wina wake/ Ndikumenya ina yake Panadutsa wina wake/ naye ali ndi wina wake Mmmmmh ma Man, Eeeh!/ Ndi Ina yake Inali nthawi zanji? Unkapanga chani? Nanga zinatha bwanji? (Ndi Ina Yake) Unali ndi ndani? Amakupanga Chani? Anakuwona ndani? (Ndi Ina Yake) VERSE ONE Kale kale kunali Baibe inayake Inali Baibe ya a Frenzi athu ena ake Tinkagwirizana Heavy udziwa munthu ndi Mlamu wake Koma zinachitikazo mmm ndi ina yake Anandikhola kwawo tsiku lina lake Ati ndivaye afuna akandithoke zina zake Nditavayako nnapezako kuli Mdala yake Nnangonamizira kufunsa Map udziwa ina yake After time Nnalandilanso phone yake Ati nditha kuvaya Mdala wayendera yake Ma Guy ambiri akuti (baibe’yo ndi ndani dzina lakee!!) Easy, nditchula dzina mwina nyimbo ina yake CHORUS VERSE TWO Tsiku lina ndikuyenda Mntauni penapake Man anandikodola akuyitana mkazi wina wake Ine kuvaya, nnampeza iye ali ndi nzake Koma sinnadziwe kuti ngini yake ndi Ina yake Boh ujeni? Ndikudabwa akugwetsa nkhope yake Sinnadziwe uyu si ujeni,, ndi sister wake Akuti ndi ma twins, ndangomva kwa nzake Mmmmmm ngini yake man, ndi ina yake Nde ndadziwa kuti uyuy ndi sister wake Ndayamba kumfunsira wandipatsa nambala yake Ndamuuza kuti tikumane mawa penapake Tizamenye inayake,, udziwa,, ina yake CHORUS VERSE THREE Ngini yayamba kuyenda boh yafika pa chimake Nzanga uja ndi ujeni, ine ndi twin sister wake Kuyenda limodzi, kuphaka life thaimu ina yake Komano ngini inazashupha Tsiku lina lake Nnavayanso kwawo day ina mwa mwambo wake Anandisekelera udziwa khalidwe lake Tinatengana yathu ija kuvaya penepake Wandigwira-ndamugwira basitu,, inayake Frenzo anatulukira naye ali ndi Baibe yake Baibe’yo ikungolira itangomuwona sister wake Akuti ndalakwitsa uyuyu ndi sister wake Koma frenzo naye anali atamenya kale inaya yake CHORUS- Till song ends All rights reserved (2014-Blakajk)
Posted on: Mon, 20 Oct 2014 18:03:11 +0000

Trending Topics



/div>

Recently Viewed Topics




© 2015