NGATI UKUFUNA MAMUNA WAKO AKUKONDE KWAMBIRI MOSAKUKAIKIRA TSATIRA - TopicsExpress



          

NGATI UKUFUNA MAMUNA WAKO AKUKONDE KWAMBIRI MOSAKUKAIKIRA TSATIRA ZINA MWA IZI! 1. Tamupatse zosowa/zofuna zake 2. Mwamuna amafunika kumunyengelera ngati mwana. 3. Tamupatse password yako apo ndiye mwamuna akukonda ndipo sadzakukaikira. 4. Tamudzudzule mwachikondi pomwe walakwitsa 5. Usapange mpikisano ndi mwamuna wako palipose iwe khala ogonja. 6. Kwa inu amene muli pa banja mammawa kukacha tamupatse mwadzuka bwanji #adad (apo nde amamva kukoma mwamuna) 7. Kwa inu apa banja ukawona mwamuna wako wachoka ku vep wangofikira direct kuchipinda ziwa zoti chilipo chomwe akufuna siya kaye zomwe umapanga mtsatire kuchipinda konko ukamve 8. Kwa inu apa banja mwamuna asayese kumakufunsa zoti akufuna kudya chakudya, ayiiiii ziwa wekha zoti #Dad apa njala yawapora ndipange chakudya (osamayiwala nkomya iyayi, kumutero mamuna wamutha) 9. Kwa inu apa banja tayesetsani mwamuna wanuyo kumpatsa respect yokwanira ngakhale ali pa gulu la anthu uyenera kumpatsa kachikondi pangono. Akazi inu dziwani izi, mamuna samakukonda ngati sumupatsa #treatment yabho, kenako mumayamba kuyankhula kuti Men are all the same kupanga update ma status nkati, Chakuda chimakulumani just because njira simuzitsata muli nganganga pamwamba pa mwanuma nthawi zonse mumafuna mwamuna azigonja inu patsogolo. Ndikukuuzani mzalira nazo mukungolumidwa ndizakuda. Mudzafa imfa yowawa ndithu! Okumva amatolapo kenakake, osamva amanyozera kapena kutukwana! Ndidzidya kaye #Coconut_Biscuit wangayu, Ndili pompa ngati uli ndi funso tafunsa! #TrixX
Posted on: Sat, 19 Jul 2014 17:26:32 +0000

Trending Topics



Recently Viewed Topics




© 2015