NKHANI YA CHISONI.mwambo wamaliro,a lyford chirwa,yemwe - TopicsExpress



          

NKHANI YA CHISONI.mwambo wamaliro,a lyford chirwa,yemwe ankadziwika ndi dzina loti Themba Nkosi,uchitika mawa ku Mochale ya Johannesburg nthawi ya 4 koloko madzuro.Ndipo thupi linyamuka la chiwiri kunka ku Malawi,pa ndege.A Lyford Chirwa amachokera mmudzi wa GvH chinyakula,TA Timbiri,boma la Nkhata bay.A Lyford Themba aphunzira sukulu yawo pa Nkhata bay secondary school,ndipo ankatumikira ngati Head boy.Ma bus onyamura anthu adzanyamuka 2koloko pm,kuchokera ku katlehong,sali section lomwe a Themba amakhala kupita ku Johannesburg town komwe tikasanzikane nawo,asananyamuke kupita ku Malawi.Muzimu wawo ukapumule mumutendere.R I P.
Posted on: Sat, 03 Aug 2013 06:46:28 +0000

Trending Topics



Recently Viewed Topics




© 2015