Ndikuweruka cha mma 5: 00 ndati i mtalowa mu checkers malingana - TopicsExpress



          

Ndikuweruka cha mma 5: 00 ndati i mtalowa mu checkers malingana ndikutenthaku ndione ka chakumwa. Ndaona mzanga ali busy kutenga zinthu kumalowetsa mmatumba a buluku lake, ine pofunsa chikatere a chimwene. Anangoti eee ukufuna moyo kapena ai? Ndangoona waisolola shortgun. Ine phazi thandize, kamtima kofunanso chakumwa chija kanatheratu kuti balala. Chenjezo! Ukaona wina akupanga zake musiye ndi biznes yake osafera za eni ai.
Posted on: Fri, 08 Nov 2013 16:03:39 +0000

Trending Topics



Recently Viewed Topics




© 2015