Nkhani yomvetsa chisoni-manyazi Dzulo-ana a Mzuzu - TopicsExpress



          

Nkhani yomvetsa chisoni-manyazi Dzulo-ana a Mzuzu united,amenyedwa kwambiri ndi mbuli za masapota a Bullets fc pa kamuzu stadium..3:30pm nthaw yomwe anawa amafuna kyamba trainng ku khonzekela kufinya maule-lelo. Ng onamo coach wa Bullets fc-wati masapotawo anatumidwadì kt akabwezere chipongwe chomwe adachitidwa ku mzuzu. Titamufusa-Gs wa bb,wati a mzuzu united,sadapemphe ground lomwe ndi la bullets fc coach wa nzeru-sangayankhule zopeperazi-mx kamuzu stadium ndiwa Boma-osat club. Thank u 3rd-c
Posted on: Sat, 27 Jul 2013 06:52:39 +0000

Trending Topics



Recently Viewed Topics




© 2015