Pamene Armstrong wabona (wasankha Yesu kukhala mpulumutsi wake) tiyeni tipempherere anthu awa kuti nawonso abone: 1. Blakjak (Kutukwana) 2. The Dare Devils (monga mwadzina lawo) 3. Revolver (kuimba zolaura) 4. Wendy (________fill the gap) 5. Peter (asiye zamathanyura) 6. Tay Green (ufiti) 7. Young Kay (asiye zomenya chibwezi chake makofi...mponela wabwino ngati Tina kumawupanga nkhanza sibwino) 8. Dan Lu (akapepese asiye kukonda ti ana ta secondary) 9. Natasha ndi Fatima (______________) 10. _________ Tchulani wanu. - Admin Kacheenda Moto
Posted on: Tue, 03 Sep 2013 20:37:15 +0000