Patrick James Ndikungomva zoti akuti Atupele Muluzi is wedding - TopicsExpress



          

Patrick James Ndikungomva zoti akuti Atupele Muluzi is wedding Angella pa 9 kodi mesa these two have children and they have been staying together for all these years. Is this wedding not a fund raising campaign for UDF? But if this marriage is coming ndicholinga chophimba anthu mmaso chifukwa chofuna mpando wawuponda ayise coz Malawians are not that sleepy kuti mpaka akapatse dziko mwana wakhanda kuti awononge zinthu. No matter how many times you can wed Angella, but take it from me my friend, ife tili pambuyo pawosakwatirayo mpaka 2014 woooooooo!!!!!!
Posted on: Sun, 27 Oct 2013 04:15:00 +0000

Trending Topics



/a>

Recently Viewed Topics




© 2015