Peter Forty chitsanzo choipa pamasewero a mpira Zinali - TopicsExpress



          

Peter Forty chitsanzo choipa pamasewero a mpira Zinali zochitisa manyazi masana a lero pomwe atolankhani anasekeledwa kunja kwa Kamuzu Stadium powalesa kukagwira ntchito yawo pomwe Flames ikupanga ma practice kukonzekera Mali ndi Ethiopia mu AFCON Ife sitikufuna za Peter Forty muno, iyi ndi game yofunikira kwambiri Anatero mmodzi wa anyamata yemwe analamulidwa kulesa atolankhani. Zabwino zonse Flames!!!!!!!!! #mkeki
Posted on: Thu, 13 Nov 2014 19:24:30 +0000

Trending Topics



Recently Viewed Topics




© 2015