Report----Bullets V Airbon!!!! Bullets Fc team yanga yokondedwa - TopicsExpress



          

Report----Bullets V Airbon!!!! Bullets Fc team yanga yokondedwa , yatuluka mu chikho cha Standard bank Dzuro pa Civo stadium Ma penalty ndi tean ya Airbon Rangers 9-8!!!! Bullets fc yima Coachedwa ndi Mavuto Lungu kamba kakuti head coach Eliya kananji ali ku under 17 kuthandiza kusura anawa!!! Yinayamba mwambambande team ya pfukoyi , zinali zosadabwisa kuona Divason Mlozi akumwetsa chigoli pa 7 minutes first half!!! Bullets yomwe yimasowekera Sakhani Mkandaire kumbuyo yinayaka moto kuzera mwa Fisher, Victor Limbani, James Chilapodwa ndi Divason Mlozi!! Paka chigawo choyamba chinatha bullets yikusewera mwa mbambande koma wosapeza chigoli china!!! Chigawo chachiwiri Bullets yinapitiliza pomwe yinalekera mu first half koma zithu zinaza sitha, Mavuto Lungu atatu lutsa Bashil Maunde, kulowesa Jet Lee kanyenda kutulutsa Dagras Chilambo ndi James Chilaponda , Bullets yinayamba kuvutika!! Zinali zosadabwitsa kuona airbon yikupeza chgoli kuti yikhale 1__1!!!! Zitathera chocho yinali thawi yama penate!!! Bullets yinamwetsa ma penalty 8 ndipo Airbon 9 kuti airbon yipitilire mu chikhochi!!! Matsiku sakoma onse zimachitika !! All the best airbon!!! Maso pa tsogolo Mnaulle!! Moto kuti buuuuuuuuuuuu!!! Tigers ndinyamure!!! !! Waganyu ndine!!! SMs BB kuy 1515!!! Mr Jabu!!! Mawa wabwino!!!
Posted on: Fri, 15 Aug 2014 05:01:33 +0000

© 2015