Timu Ya Mzuzu University FC yomwe imamenya mu Simama Northern - TopicsExpress



          

Timu Ya Mzuzu University FC yomwe imamenya mu Simama Northern Region Football League yapeza chithandizo(Sponsorship) kuchokera ku kampani ya SEEDCO MALAWI LTD. Mmbuyomu timuyi imathandizidw ndi Sukulu yomweyi ya Mzuzu University koma tsopano china chilichonse idzithandiza ndi kampani ya Seedco. Ndipo Mkulu wa Mzuni wathokoza kampani ya Seedco poonetsa chitsanzo chabwino kumakampani ena pochita zimenezi.
Posted on: Thu, 31 Jul 2014 07:48:47 +0000

Trending Topics



Recently Viewed Topics




© 2015