Umphawi uwu ndi owuputa dala munthu ulibe malaya,nsapato ngakhale - TopicsExpress



          

Umphawi uwu ndi owuputa dala munthu ulibe malaya,nsapato ngakhale trouser yomwe uchita kubwereka kuchapa kudikirira iume koma mowa weekend iliyonse sulephera kumwa mpaka umaiwala kuti umakhala nyumba ya rent a landload akafunsa ndie kumaganiza zopempha anzako akubwereke ndalama ya rent and pomwe ulipo sumatha kubwenza ngongole eeeeeeeh izi simbali yathu siyana mowa guys ngati ukukuzunguzani bola mungokwatira bansi
Posted on: Tue, 30 Jul 2013 06:26:20 +0000

Trending Topics



Recently Viewed Topics




© 2015