ZIFUKWA ZOWE SINDKHILA ND CHBWENZ: 1:mkazi mmutu - TopicsExpress



          

ZIFUKWA ZOWE SINDKHILA ND CHBWENZ: 1:mkazi mmutu madred/wiv=k4,500 ine kumetesa= k70 2:mkaz pair yama g string nd ma bra=k3.500 ine ma boxer awiri ama two hanz=k400 3:mkaz ma purity pads=k1,500 ine handkachifi ya 50 ba=k50 4:mkaz akalowa ntown afuna akadye pa chichen inn @chips chken=k2,500 pomwe ine kuchimilire ndimauza mama nsima ya 50 nyemba za 30 masamba a 20 =k100 5:mkaz akafuna clubing nd chez or blues savana mmoz =k1000 ine ndikafuna ku njanja nd pa shabin red deer 70 ba phushan 50 ba mogo 30 ba =k500 umaona kalala #demeti mwaona sikut ndiuswaz @achina cfb mutchesa inuyo @nje man #yeye
Posted on: Sat, 24 Jan 2015 07:35:42 +0000

Trending Topics



Recently Viewed Topics




© 2015