a Malawi amzanga ine monga panopachema ndakhuzidwa kwa mbiri kut - TopicsExpress



          

a Malawi amzanga ine monga panopachema ndakhuzidwa kwa mbiri kut mzathu wapita mwamtundu woterewu anali msangalasi wa dziko lanthu ndikuthuthumira ndi matha kut kodi anthu anthu otchuka azipita moteremu Plz guys tiyeni tikhale okonzeka paja mau amat kwasala tchire ndikomwe moto ulowera iye sazabwera kuno koma ife kumusatira komko koma njira yabwino ndikuzapitako titamulandira Yesu kut alamulire moyo wanthu
Posted on: Mon, 12 Aug 2013 12:11:50 +0000

Trending Topics



Recently Viewed Topics




© 2015