after Bingus era, every Malawian thought the Daniel Phiri Paulendo - TopicsExpress



          

after Bingus era, every Malawian thought the Daniel Phiri Paulendo (DPP) gafferment would learn from their mistakes and do the needful, that is embracing accountability and transparency, and prioritize zinthu zothandiza fuko la Malawi like health, education, water, agriculture. Koma just under 6 months of existence ayamba kale depriving these sectors: 1) Kuba ndalama za National AIDS Commission (NAC); 2) Kuba ndalama za Central Medical Stores akuti donation ya ma dust bins. The City Assembly has struggled over the years to have such gestures koma awa anantchathuwa adala chotani lero ndi lero? 3) Malata ndi simenti subsidy. Kufuna kungobapo ndalama from suppliers to distributors kuti zipite ku Mlakho ndi tima scrupulous business persons onamizila kuti ndi ma wellwishers; 4) Dubious presidential advisors. Kumangochita dzima appointments anthu ambiri mbiri for political appeasement to Daniel Phiri Paulendo (DPP) sympanthisers Just six months in office, things are back to worse times like it was before April 2012! Mukaona 2015 another 20 July nkhani zake ndi matsoka a boma lobera ili la BWAMPINI! Bwerani ma cadets, ntchito iyi ili apayi. Defend your drunken spent professor! ACHOKEEEEEEEEEEE
Posted on: Wed, 24 Dec 2014 12:49:13 +0000

Trending Topics



Recently Viewed Topics




© 2015