bambo ndi mayi akunyumba kuwerenga magazine, Bambo “oowooh no - TopicsExpress



          

bambo ndi mayi akunyumba kuwerenga magazine, Bambo “oowooh no eti serena williams ali mpathupi??..azibambo ena ndi amwayi..ife mpaka titapangatu resign ucashierwu kuti timtakase mosalekeza..mwachiona chimwendo!!amayitioneko..page chani?kamamunake ndi aka?abambo a lazah mpakeekah..or ntakhala ine pomatha 1week tili limodzi katatsala chikhadabo chakumwendo..kuntundaku ntakatafuna-tafuna ine kamamuna ka...khofi..khofi..khofi mbale ndi magazine kuti mbwerekete
Posted on: Fri, 04 Jul 2014 18:30:19 +0000

Recently Viewed Topics




© 2015