ku Malawi ndikwabwino and mitundu yonse ya anthu kumudzi - TopicsExpress



          

ku Malawi ndikwabwino and mitundu yonse ya anthu kumudzi ngakhale mtown anthu ndi aulemu wawo koma chomwe chandikhudza kuti ndiyankhule ndi ichi wina wake dzulo amanyoza mtundu wa ayao kuti ndi mbuli sapita kusukulu zimene zingowonetselatu kusoweka mkhalidwe munthu kunyoza anthu a fuko lakwao penapake abale pokomentela zinthu tiziotsetsa kuti ku ayaoko kulibe wina wachibalee?! popezanso atumbuka amene mumati ndi anzelu tikuwaona moyendamu akudyanso malilime pamaso pa azungu ndi amwenye payankhula muzibweza moto muzidziwa mukuyankhula ndiwanthu.
Posted on: Fri, 27 Sep 2013 12:31:48 +0000

Trending Topics



Recently Viewed Topics




© 2015