that tense moment: When after training hard for three weeks the - TopicsExpress



          

that tense moment: When after training hard for three weeks the coach calls the team to name his travelling squad and says: tikanankonda tikanakhala tonse .. koma a boma akuti alibe ndalama nde titenge anthu 18. omwe mutasalenu you are still part of the team osadandaula tikabwerako tizakutiyitananinso.Choncho omwe tikupita nawo kunja ndi as follows:....... umangoziwiratu kuti DROPPED kapena kuti wakunyumba.. AZZURI
Posted on: Thu, 03 Oct 2013 08:47:34 +0000

Trending Topics



Recently Viewed Topics




© 2015