vuto LA a Malawi ndiloti akukaksmizidwa kumasewela nawo mipila - TopicsExpress



          

vuto LA a Malawi ndiloti akukaksmizidwa kumasewela nawo mipila yomwe cholinga chair chosewelera sakuchidziwa.akudziwa maseweledwe yes koma akasewela mpila uja allowance mk 4 pin pamene player ngati yomweyo kunjako game allowance amagula galimoto kumamwa champagne nyumba yabwino athuwa tikudyela limodzi mbatata my katawamu/kawale/ndilande .NDE muziti Malawi imenya yes imenyadi koma mgaiwa nkumakodzela makoma a mipanda mmbali mwa miseu imeneyo yokhayo yomakodzakodzayo timaitha shutuppppp
Posted on: Mon, 13 Oct 2014 20:46:11 +0000

Trending Topics



Recently Viewed Topics




© 2015