1: Kachasu botolo la koko- MK150 Squash pure water-MK300 *Kenako - TopicsExpress



          

1: Kachasu botolo la koko- MK150 Squash pure water-MK300 *Kenako mumati anyamata amasiku ano amakonda mowa*. 2:Chamba- MK30 Cholembela - MK50 *Nde muziti ana amasuta kwambiri masiku ano*. 3:Disco - MK300 Show ya church - MK2500 *kenako mumati tinataika, sitikonda ma show a mu church*. 4:Magazine- MK200 Ma book aku school - MK3000 *Kenako mumati sitikonda kuwelenga za xul* 5:chibwenzi-k5000 yaku saloon hule- k500 ndiye muziti ife tikukonda mahule..... 6:mkaka k200 ,sachet k60 nde muzit timakonda masachet * Skin-jin =k1200 Suit ya anyamata (DB) =k13,000 *Kenako mumati timakonda kuvala zovala zothina* Legins =k600 Suit =k10,000 *Kenako mumati mwana wa ujeni uja ndi Hule coz amakonda kuvala ma legns* Kumetetsa MK 500, Afro freee * nde muziti anyamata a masiku ano sameta* Mukufuna chani kweni-kweni???
Posted on: Sun, 25 Jan 2015 11:08:42 +0000

Trending Topics



Recently Viewed Topics




© 2015